Tsar Cris

Tsar Cris Content Creator, Blogger, Journalist, Videographer, Photographer, Graphic Designer, Website Developer, Podcaster under Mindset Entertainment

18/09/2026

Koma bwana Monera mwadandaulatu koma ntendere akupeza ameneyo link in comments section

Nde Chikadzati. Komabe unkaziwabe, alipo ukumukonda eeeh, koma kundikakamira ndikhalebeeeZikuoneka kuti chi nyimbo chipo...
15/09/2026

Nde Chikadzati. Komabe unkaziwabe,
alipo ukumukonda eeeh,
koma kundikakamira ndikhalebeee
Zikuoneka kuti chi nyimbo chiposa chija akhala akuchigwetsa pompano koma Zi ana izi

Koma ichi mumatchula kuti chi Eli Njuchi ndichidolo chikugwetsa Extended Playlist akuti Maga iyi itha kuzakhala Album of...
15/09/2026

Koma ichi mumatchula kuti chi Eli Njuchi ndichidolo chikugwetsa Extended Playlist akuti Maga iyi itha kuzakhala Album of the year mukuona bwanji
EP 25/09/2026

14/09/2026

Ii koma ichiiii

14/09/2026

Koma uyu ndidolo kwambiri. Chi Chinyimbo kuchoka kwa Bicon Mw akuti Kakamira koma ofunika chiiikidwe pa repeat https://youtu.be/7da5JG255rg

Mwina simukuziwa we have international level yomwe yafikaInu mukuganiza kuti anthuwa ndioyenera kapena avoteso
13/09/2026

Mwina simukuziwa we have international level yomwe yafika

Inu mukuganiza kuti anthuwa ndioyenera kapena avoteso

Address

Midima Road
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tsar Cris posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share