08/08/2026
olemekezeka a George kasakula Spotted Ku Maliro Kwa Brian Banda
Let's Connect
08/08/2026
olemekezeka a George kasakula Spotted Ku Maliro Kwa Brian Banda
08/08/2026
eeee zinthu zake
inde Masiku Sakoma Ose
komarelori lanyanya
mmm😭😭😭
08/08/2026
Mr President pobwera adzapeza Brian Banda kulibe 💔🕊️
08/08/2026
Mwina vuto ndineyo koma uyuyu moopa mulungu uyuyu samasekesa🚮🚮💔.
Politics is a dirty game.
It’s do or die.
Umatha kuluza moyo. 🥀
(zambili zikuchitika kunjaku)
08/08/2026
Rest In Eternal Peace Brian Banda
tikusowani😭😭😭
(Adangogwa pampando kuthamangila naye kuchipatala akut mwabweretsa muthu wakufa)
Cheeiii😭😭😭😭
08/08/2026
Limodzi la Pemphero limene Mulungu anakanitsitsa kuliyakha...
08/08/2026
Kalibu Nzimbe yokoma iyi🫘?
08/08/2026
Tatiyankeni fuso ili azimayi komaso odziwa kuphika
👇👇👇