Kena Kake Vibez

Kena Kake Vibez

Share

Where the wild stuff lives 🔥
Music | Memes | Trends | Gist
Mw only 🇲🇼

20/07/2026

Good morning neba 😁😅

18/07/2026

HAPPY BIRTHDAY MKULUKUTA MOYO 😁🎊 mau amodzi kwa Mr President??

17/07/2026

Ati anamufunsa Meta Ai zokhudza Waxy Kay 🤧😅🙌

16/07/2026

Tangotelo madzulo ano! Kalibu 😁🤓

16/07/2026

AYI ZIKAMATELE BWENZI ZIKOMA 🤧😁

Sopano pano Akaidi onse ku ndende ya Chichiri ku Blantyre ayamba kudya katatu pa tsiku zomwe sizinayambe zachitikako.

Ndipo Akaidi ali okondwera kwambiri pa upangili umenewu 🤓

abale zabwino zipose apa??

16/07/2026

Achina iwe ndiine mpaka M'manda pano muli manda ake ati Kodi?😂💔🙈🏃

16/07/2026

From inbox
Ndine ka mnyamata ka zaka 34 ndimakhala kwa sister wanga koma mwamuna wake amandipanga nkhaza🥴🥴😭 Nditani gyz?😭

15/07/2026

Alamu anu akati akazinge 😁🤓
Nkhomaliro yabwino kaya Inu mwakonza zotani kumeneko!!?

15/07/2026

Komatu bwenzi mwadzuka kuzizila kuli apo 🤧 nanga olo 5sau muli nayo Inu 🙄😒

14/07/2026

Boma Lapita Lija Kutaya Mowa Ogula Wekha Umamenyedwaso 🙌💔🤣

Want your school to be the top-listed School/college?

Website