Machilitso M'chisilamu

Machilitso M'chisilamu Answer the questions that will be asked here and stand a chance of winning Airtime

20/04/2022

Bismillah Rahman Rahim
AlGaffar =The forgiving

Frequently recited Allah will remove Love of the world from his heart, and will have a good death.

M'dzina la Allah wachifundo komanso chisoni chambiri.

AlGaffar= Okhuluruka
Kutchula pafupi pafupi dzina limeneli Allah adzamuchotsera Munthu kukonda za mdziko ndipo azapanga imfa yake kukhala yofewa.

20/02/2022


Kod mumadziwa k*t dzina limeneli ndi lalikulu kwambiri?
Munthu amene angatchule dzina limeneli mobwerezabwereza ka 1000 ,
Mulungu adzayeretsa mtima wake kuchokera ku zoipa.
Komanso munthu amachira ku mnthenda yosachizika. Akuyenera k*tchula mnthenda imene akudwala ndikupempha kwa
Mulungu ndipo mwachifuniro cha Mulungu iye adzachila

22/12/2021

Those who answered correctly their names Will be mentioned here.
The lucky winners of last week's question will receive their reward in this week.
Inshallah

05/12/2021

Today's question
What does the word Quran mean?

Funso lathu la lero
Kodi mau ok*ti Quran amatanthauza Chan?
Remember: if you answered correctly you may have a chance of winning airtime
+265 only🇲🇼

29/11/2021

Invite your friends to like this page
To reach 100likes.
And soon we are going to asking questions so that you may stand a chance of winning airtime

25/11/2021

Tomorrow we're going to start asking questions..
Invite your friends to like our page and you will be among the 5 lucky winners of airtime

24/11/2021

Pangani like page iyi
Osati post

23/11/2021

بسم الله الر حمن الر حيم
Lachisanu tiyamba kufunsa mafunso ..
Ndipo anthu 5 amwai azilandila airtime
Pangani like page iyi k*t muzilandira mafunso

Address

Blantyre

Telephone

+265996263113

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Machilitso M'chisilamu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Machilitso M'chisilamu:

Shortcuts

Share