Jacqueline Dikamdima mlakatuli

Jacqueline Dikamdima mlakatuli

Share

we left home,,,, to change home,,,,,, don't forget the goal

27/10/2024

27/10/2024

Am good at doing two things. 1 is to mind my business, and 2 is to respect other people and at the same time am good at defending myself 🥳

Photos from Jacqueline Dikamdima mlakatuli's post 27/04/2024

Last born wamayanga...... lero kwangocha ndizisomo basi.... nanuso muzingosekera mulungu ndodabwitsa

27/04/2024

Nde pali chikondi cha automatic thupi limakana koma mtima umakakamiza for no reason 🤣🤣🤣🤣🤣

Mwadzuka bwanji kumeneko

Photos from Jacqueline Dikamdima mlakatuli's post 12/03/2024
06/02/2024

It's a beautiful morning

15/10/2022

happy mothers day to all mothers

23/09/2022

Ngat chiri chizolowezi chako kuseweretsa mtima wazimayi ngat mpira lero ndikuuza chirungamo

Mwadzuka bwanji PL

21/09/2022

Kunja kwacha....... Atsikanafe tiyambepo kusakasaka ntchito,,, tiyambe kumva mabwana mma office mu Ati ntchito iripo ubwere mma 6pm Ku ...... Lodge for interviews mmmmmmmmm mwatani mabwana?..

Mwadzuka bwanji Poet lovers

17/09/2022

Kodi mukamati ndiri Ku high way mumanena mutimo chifukwa akati high ananduza kuti chichewa chake ndi m'mwamba nde ine high way kumalawi kuno sinnadutsepo uli kuti makamaka....... # mwadzuka bwanji uko

15/09/2022

Mwadzuka bwanji PL..... CHULUKECHULUKE NGWA NJUCHI UMANENA IYO YAKULUMA KOMA YOMWE INANDILUMA TSIKU LIMENERO SINNAYIWONE CHIFUKWA NDINALI OGULITSA THUPI

MUNAYIMVERA KALE IYI????

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address

Blantyre