Talk it out with Dr. Patrick Bande

Talk it out with Dr. Patrick Bande Dr Bande is a Pan-African scholar and a free thinker from Malawi to the World. A social activist and China expert.
(3)

If you follow my page be prepared to see different perspectives to issues. I may question your beliefs, so be prepared for such moments.

Top fan wanyumba momunoMan Richard
03/09/2026

Top fan wanyumba momuno
Man Richard

All the way from Salima...Achibale
03/09/2026

All the way from Salima...Achibale

Kodi Aubrey uja business ikuyenda bwanji?Timusatile kuti timve feedback?...chifukwa ena ayamba kunong'ona akuti ma chick...
03/09/2026

Kodi Aubrey uja business ikuyenda bwanji?
Timusatile kuti timve feedback?...chifukwa ena ayamba kunong'ona akuti ma chick kwambiri Aub... Sweet talker 🤣😂

Mwamukumbukira dolo uyu?Anandipatsa update kuti a Insurance adamupeza ndikusayinitsa mapepala kuti akupatse zake ....nkh...
03/09/2026

Mwamukumbukira dolo uyu?
Anandipatsa update kuti a Insurance adamupeza ndikusayinitsa mapepala kuti akupatse zake ....nkhani yabwino, we hope walandira pano

03/09/2026

Kwavuta ku Malawi..... koma Suleiman alandile Ulemu

02/09/2026

Shaa!

Ku Malawi kuli tiwanthu tongokonda kutsutsa ndikutayitsana nthawi ndi ma arguments opusa.Ndakuuzani kuti mzimayi uyu mme...
02/09/2026

Ku Malawi kuli tiwanthu tongokonda kutsutsa ndikutayitsana nthawi ndi ma arguments opusa.

Ndakuuzani kuti mzimayi uyu mmene amapezaMankhwala amalungo 1969 analibe degree ya medicine ndipo analibe PhD.

Ndiye basi tima argument tanu tazi, chipongwe mkati....ena atombolombo ati iwowo adaphunzira zachipatala ndiye akuyiziwa story ya mayiwa kuposa ineyo...

Sitidanene kuti mpaka lero mayiwa sadapangenso maphunziro kapena kupita kunja ayi, koma 1969 pamene amapanga zimenezi adali asaphunzirepo kunja kwa China.

Osamachita phuma

02/09/2026

Asilikali a America afika ku Thailand kukasangalala kaye...kuchotsa nthukutira😂🤣

NKHANI MWACHIDULEIran ikuti sitima ziwiri zonyamula mafuta zabuka moto ku strait of Hormuz zitagunda mabomba otcheledwa ...
02/09/2026

NKHANI MWACHIDULE

Iran ikuti sitima ziwiri zonyamula mafuta zabuka moto ku strait of Hormuz zitagunda mabomba otcheledwa pa madzi ndipo zikuyaka padakali pano.

Dziko la Peru, lalengeza kuti lathetsa ubale waukazembe ndi dziko la Iran kamba koti dziko la Iran likusokoneza ntchito za mtengatenga pa madzi komanso likuyambitsa nkhondo ku middle east.

Dziko la Peru limapezeka ku South America ndipo kukhala ngati latenga mbali ya Donald Trump.

02/09/2026

Ndizoona kwathu kuno kwagwa mvula yochuluka, koma mumzinda womwe kuli ine Black Teacher kulibe ma floods padakali pano. Ma floods mukuona mu video Ali ku mzinda wina kutali ndi kwathu kuno koma chigawo chofanana. Zikomo pokhala okhuzidwa

Address

23 Victory Close
Blantyre
DH87FB

Telephone

+265997406096

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Talk it out with Dr. Patrick Bande posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The School

Send a message to Talk it out with Dr. Patrick Bande:

Shortcuts

Share

Category